-
Nyimbo ya Solomo 7:8Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
8 Ine ndinanena kuti, ‘Ndikwera mtengo wa kanjedza
Kuti ndikathyole nthambi zake zokhala ndi zipatso.’
Mabere ako akhale ngati phava la zipatso za mpesa,
Ndipo mpweya wamʼkamwa mwako ununkhire ngati maapozi,
-