Nyimbo ya Solomo 8:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 “Ndikulakalaka ukanakhala mchimwene wanga,Amene anayamwa mabere a mayi anga. Ndikanakupeza panja, ndikanakukisa,+Ndipo palibe amene akanandinyoza.
8 “Ndikulakalaka ukanakhala mchimwene wanga,Amene anayamwa mabere a mayi anga. Ndikanakupeza panja, ndikanakukisa,+Ndipo palibe amene akanandinyoza.