-
Nyimbo ya Solomo 8:5Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
5 “Kodi ndi ndani amene akuchokera kuchipululuyu,
Atakoleka dzanja lake mʼkhosi mwa wachikondi wake?”
“Ine ndinakudzutsa pansi pa mtengo wa maapozi.
Pamenepo mʼpamene mayi ako anamva zowawa pokubereka.
Mayi amene anakubereka anamva zowawa ali pamenepo.
-