-
Nyimbo ya Solomo 8:9Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
9 “Akakhala khoma,
Timʼmangira kampanda kasiliva pamwamba pake,
Koma akakhala chitseko,
Timʼkhomerera ndi thabwa la mkungudza.”
-