Nyimbo ya Solomo 8:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Solomo anali ndi munda wa mpesa+ ku Baala-hamoni. Munda wa mpesawo anaupereka kwa anthu oti aziusamalira. Ndipo munthu aliyense ankabweretsa ndalama zasiliva zokwana 1,000 zolipirira zipatso za mundawo.
11 Solomo anali ndi munda wa mpesa+ ku Baala-hamoni. Munda wa mpesawo anaupereka kwa anthu oti aziusamalira. Ndipo munthu aliyense ankabweretsa ndalama zasiliva zokwana 1,000 zolipirira zipatso za mundawo.