-
Nyimbo ya Solomo 8:12Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
12 Ndili ndi munda wanga wa mpesa umene ndingathe kuchita nawo chilichonse chimene ndikufuna.
Ndalama 1,000 zasilivazo ndi zanu inu a Solomo,
Ndipo ndalama zasiliva 200 ndi za anthu amene amasamalira zipatso za mundawo.”
-