Yesaya 1:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Tsoka kwa mtundu wochimwa,+Anthu olemedwa ndi zolakwa,Ana a anthu ochita zoipa, ana a makhalidwe oipa. Iwo asiya Yehova.+Achitira Woyera wa Isiraeli zinthu zopanda ulemu.Iwo atembenuka nʼkumusiya. Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 1:4 Yesaya 1, ptsa. 14-15 Nsanja ya Olonda,10/15/1987, tsa. 12
4 Tsoka kwa mtundu wochimwa,+Anthu olemedwa ndi zolakwa,Ana a anthu ochita zoipa, ana a makhalidwe oipa. Iwo asiya Yehova.+Achitira Woyera wa Isiraeli zinthu zopanda ulemu.Iwo atembenuka nʼkumusiya.