Yesaya 1:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Imvani mawu a Yehova, inu olamulira ankhanza a ku Sodomu.+ Mvetserani malamulo* a Mulungu wathu, inu anthu a ku Gomora.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 1:10 Yesaya 1, tsa. 22
10 Imvani mawu a Yehova, inu olamulira ankhanza a ku Sodomu.+ Mvetserani malamulo* a Mulungu wathu, inu anthu a ku Gomora.+