Yesaya 1:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Mzinda wokhulupirika+ uja wasanduka hule.+ Unali wodzaza ndi chilungamo+Ndipo zachilungamo zinkakhala mwa iye,+Koma tsopano muli zigawenga zopha anthu.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 1:21 Yesaya 1, ptsa. 29-31
21 Mzinda wokhulupirika+ uja wasanduka hule.+ Unali wodzaza ndi chilungamo+Ndipo zachilungamo zinkakhala mwa iye,+Koma tsopano muli zigawenga zopha anthu.+