Yesaya 1:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Ziyoni adzawomboledwa ndi chilungamo+Ndipo anthu ake amene adzabwerere, adzawomboledwanso ndi chilungamo. Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 1:27 Yesaya 1, ptsa. 33-34
27 Ziyoni adzawomboledwa ndi chilungamo+Ndipo anthu ake amene adzabwerere, adzawomboledwanso ndi chilungamo.