Yesaya 1:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Chifukwa mudzakhala ngati mtengo waukulu umene masamba ake akufota,+Ndiponso ngati munda umene ulibe madzi. Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 1:30 Yesaya 1, tsa. 35 Nsanja ya Olonda,10/15/1987, tsa. 12
30 Chifukwa mudzakhala ngati mtengo waukulu umene masamba ake akufota,+Ndiponso ngati munda umene ulibe madzi.