-
Yesaya 1:31Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
31 Munthu wamphamvu adzakhala ngati udzu wouma,
Ndipo ntchito yake idzakhala ngati kamoto kakangʼono.
Zonsezi zidzayakira limodzi
Popanda wozizimitsa.”
-