Yesaya 2:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Inu mwasiya anthu anu, nyumba ya Yakobo,+Chifukwa iwo ayamba kutsatira miyambo yambiri ya Kumʼmawa.Akuchita zamatsenga+ ngati AfilisitiNdiponso ali ndi ana ambiri a alendo. Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 2:6 Yesaya 1, ptsa. 49-50
6 Inu mwasiya anthu anu, nyumba ya Yakobo,+Chifukwa iwo ayamba kutsatira miyambo yambiri ya Kumʼmawa.Akuchita zamatsenga+ ngati AfilisitiNdiponso ali ndi ana ambiri a alendo.