Yesaya 2:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Dziko lawo ladzaza ndi siliva komanso golide,Ndipo ali ndi chuma chopanda malire. Dziko lawo ladzaza ndi mahatchi,Ndipo ali ndi magaleta osawerengeka.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 2:7 Yesaya 1, ptsa. 50-51
7 Dziko lawo ladzaza ndi siliva komanso golide,Ndipo ali ndi chuma chopanda malire. Dziko lawo ladzaza ndi mahatchi,Ndipo ali ndi magaleta osawerengeka.+