-
Yesaya 2:13Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
13 Lidzafikira mikungudza yonse ya ku Lebanoni yomwe ndi yonyada komanso yodzikweza.
Lidzafikiranso mitengo ikuluikulu yonse ya ku Basana,
-