Yesaya 2:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Anthu adzalowa mʼmapanga a muthanthweNdiponso mʼmayenje a munthaka,+Chifukwa cha kuopsa kwa mkwiyo wa YehovaNdiponso chifukwa cha ulemerero wake waukulu+Akaimirira kuti achititse dziko lapansi kunjenjemera ndi mantha. Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 2:19 Yesaya 1, ptsa. 53-56
19 Anthu adzalowa mʼmapanga a muthanthweNdiponso mʼmayenje a munthaka,+Chifukwa cha kuopsa kwa mkwiyo wa YehovaNdiponso chifukwa cha ulemerero wake waukulu+Akaimirira kuti achititse dziko lapansi kunjenjemera ndi mantha.