-
Yesaya 2:21Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
21 Kuti abisale mʼmayenje a mʼmatanthwe
Ndi mʼmingʼalu ya mʼmiyala ikuluikulu,
Chifukwa cha kuopsa kwa mkwiyo wa Yehova
Ndiponso chifukwa cha ulemerero wake waukulu
Akaimirira kuti achititse dziko lapansi kunjenjemera ndi mantha.
-