-
Yesaya 2:22Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
22 Kuti zinthu zikuyendereni bwino, siyani kudalira munthu wamba,
Amene ali ngati mpweya chabe wa mʼmphuno mwake.
Kodi pali chifukwa chilichonse choti munthu azimudalira?
-