Yesaya 3:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Tsiku limenelo iye adzakana nʼkunena kuti: “Ine sindikufuna kukhala womanga* zilonda zanu.Mʼnyumba mwanga mulibe chakudya kapena zovala. Musandiike kuti ndikhale wolamulira anthuwa.” Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 3:7 Yesaya 1, ptsa. 56-57
7 Tsiku limenelo iye adzakana nʼkunena kuti: “Ine sindikufuna kukhala womanga* zilonda zanu.Mʼnyumba mwanga mulibe chakudya kapena zovala. Musandiike kuti ndikhale wolamulira anthuwa.”