Yesaya 4:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Yehova akadzatsuka nyansi* za ana aakazi a Ziyoni+ ndiponso akadzatsuka magazi amene Yerusalemu anakhetsa, pogwiritsa ntchito mzimu wa chiweruzo komanso mzimu woyaka moto,+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 4:4 Yesaya 1, ptsa. 69-70
4 Yehova akadzatsuka nyansi* za ana aakazi a Ziyoni+ ndiponso akadzatsuka magazi amene Yerusalemu anakhetsa, pogwiritsa ntchito mzimu wa chiweruzo komanso mzimu woyaka moto,+