Yesaya 5:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ndidzangousiya kuti ukhale munda wosalimidwa.+Sindidzatengulira mitengo yake kapena kuulima. Mʼmundamo mudzamera zitsamba zaminga komanso tchire,+Ndipo ndidzalamula mitambo kuti isagwetse mvula pamundawo.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 5:6 Yesaya 1, tsa. 78
6 Ndidzangousiya kuti ukhale munda wosalimidwa.+Sindidzatengulira mitengo yake kapena kuulima. Mʼmundamo mudzamera zitsamba zaminga komanso tchire,+Ndipo ndidzalamula mitambo kuti isagwetse mvula pamundawo.+