Yesaya 5:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Choncho Manda* akulitsa malo akeNdipo atsegula kwambiri pakamwa pake kupitirira malire.+Anthu olemekezeka a mumzindawo, khamu lake limene limachita phokoso komanso zikondwerero zakeAdzatsikira mʼmandamo.
14 Choncho Manda* akulitsa malo akeNdipo atsegula kwambiri pakamwa pake kupitirira malire.+Anthu olemekezeka a mumzindawo, khamu lake limene limachita phokoso komanso zikondwerero zakeAdzatsikira mʼmandamo.