-
Yesaya 5:17Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
17 Kumeneko, ana a nkhosa amphongo adzadyako msipu ngati kuti ali pamalo odyetserapo ziweto.
Alendo adzadyera mʼmabwinja mmene kale munali nyama zodyetsedwa bwino.
-