-
Yesaya 5:27Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
27 Pakati pawo palibe aliyense amene watopa kapena amene akupunthwa.
Palibe amene akuwodzera kapena amene akugona.
Lamba wa mʼchiuno mwawo sanamasulidwe,
Ndipo zingwe za nsapato zawo sizinaduke.
-