-
Yesaya 7:18Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
18 Pa tsiku limenelo, Yehova adzaimbira likhweru ntchentche zimene zili mʼmitsinje ingʼonoingʼono yakutali yotuluka mumtsinje wa Nailo ku Iguputo komanso njuchi zimene zili mʼdziko la Asuri.
-