Yesaya 7:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Pa tsiku limenelo Yehova adzakumetani tsitsi la kumutu ndi tsitsi la mʼmiyendo pogwiritsira ntchito lezala lobwereka la kuchigawo cha ku Mtsinje,* pogwiritsira ntchito mfumu ya Asuri,+ ndipo lezalalo lidzametanso ndevu zanu. Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 7:20 Yesaya 1, tsa. 110
20 Pa tsiku limenelo Yehova adzakumetani tsitsi la kumutu ndi tsitsi la mʼmiyendo pogwiritsira ntchito lezala lobwereka la kuchigawo cha ku Mtsinje,* pogwiritsira ntchito mfumu ya Asuri,+ ndipo lezalalo lidzametanso ndevu zanu.