-
Yesaya 7:22Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
22 Chifukwa cha kuchuluka kwa mkaka, iye azidzadya bata, chifukwa bata ndi uchi nʼzimene munthu aliyense wotsala mʼdzikolo azidzadya.
-