Yesaya 9:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Chifukwa mwathyolathyola goli la katundu wawo,Ndodo yomwe inali pamapewa awo, ndodo ya amene ankawagwiritsa ntchito,Ngati pa tsiku limene Amidiyani anagonjetsedwa.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 9:4 Yesaya 1, ptsa. 128-129
4 Chifukwa mwathyolathyola goli la katundu wawo,Ndodo yomwe inali pamapewa awo, ndodo ya amene ankawagwiritsa ntchito,Ngati pa tsiku limene Amidiyani anagonjetsedwa.+