Yesaya 9:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Siriya adzachokera kumʼmawa ndipo Afilisiti adzachokera kumadzulo,*+Iwo adzadya Isiraeli ndi pakamwa potsegula.+ Chifukwa cha zonsezi, mkwiyo wake sunabwerere,Koma dzanja lake lidakali lotambasula kuti awalange.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 9:12 Yesaya 1, ptsa. 134, 136-137
12 Siriya adzachokera kumʼmawa ndipo Afilisiti adzachokera kumadzulo,*+Iwo adzadya Isiraeli ndi pakamwa potsegula.+ Chifukwa cha zonsezi, mkwiyo wake sunabwerere,Koma dzanja lake lidakali lotambasula kuti awalange.+