Yesaya 9:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Munthu wachikulire komanso wolemekezeka kwambiri ndi amene ali mutu,Ndipo mneneri wopereka malangizo abodza ndi amene ali mchira.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 9:15 Yesaya 1, ptsa. 137-138
15 Munthu wachikulire komanso wolemekezeka kwambiri ndi amene ali mutu,Ndipo mneneri wopereka malangizo abodza ndi amene ali mchira.+