Yesaya 10:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Kuwala kwa Isiraeli+ kudzasanduka moto+Ndipo Woyera wake adzasanduka lawi lamoto.Motowo udzayaka nʼkupsereza udzu wake komanso zitsamba zake zaminga pa tsiku limodzi. Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 10:17 Yesaya 1, ptsa. 149-150
17 Kuwala kwa Isiraeli+ kudzasanduka moto+Ndipo Woyera wake adzasanduka lawi lamoto.Motowo udzayaka nʼkupsereza udzu wake komanso zitsamba zake zaminga pa tsiku limodzi.