Yesaya 10:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Taonani! Ambuye woona, Yehova wa magulu ankhondo akumwamba,Akudula nthambi ndipo zikugwa ndi mkokomo waukulu.+Mitengo italiitali ikudulidwa,Ndipo imene ili mʼmwamba ikutsitsidwa.
33 Taonani! Ambuye woona, Yehova wa magulu ankhondo akumwamba,Akudula nthambi ndipo zikugwa ndi mkokomo waukulu.+Mitengo italiitali ikudulidwa,Ndipo imene ili mʼmwamba ikutsitsidwa.