Yesaya 13:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Nyama zakutchire zizidzalira munsanja zake,Ndipo mimbulu izidzalira mʼnyumba zake zachifumu zokongola. Nthawi yoti apatsidwe chilango yayandikira, ndipo zimenezi zichitika posachedwa.”+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 13:22 Yesaya 1, ptsa. 180-181
22 Nyama zakutchire zizidzalira munsanja zake,Ndipo mimbulu izidzalira mʼnyumba zake zachifumu zokongola. Nthawi yoti apatsidwe chilango yayandikira, ndipo zimenezi zichitika posachedwa.”+