Yesaya 14:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Mafumu ena onse a mitundu ya anthu,Onsewo anaikidwa mʼmanda molemekezeka,Aliyense mʼmanda* ake. Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 14:18 Yesaya 1, ptsa. 185-187