Yesaya 16:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Choncho Mowabu adzalira mofuula chifukwa cha tsoka lake.Aliyense wokhala mʼMowabu adzalira mofuula.+ Omenyedwawo adzalirira mphesa zouma zoumba pamodzi za ku Kiri-hareseti.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 16:7 Yesaya 1, tsa. 193
7 Choncho Mowabu adzalira mofuula chifukwa cha tsoka lake.Aliyense wokhala mʼMowabu adzalira mofuula.+ Omenyedwawo adzalirira mphesa zouma zoumba pamodzi za ku Kiri-hareseti.+