Yesaya 17:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Mizinda ya Aroweri+ idzasiyidwa.Idzasanduka malo amene ziweto zimagonaPopanda aliyense woziopseza.