-
Yesaya 17:12Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
12 Tamverani! Kuli chipwirikiti cha anthu ambirimbiri,
Amene akuchita mkokomo ngati nyanja.
Mitundu ya anthu ikuchita chipolowe,
Ndipo phokoso lawo lili ngati mkokomo wa madzi amphamvu.
-