Yesaya 18:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Chifukwa Yehova wandiuza kuti: “Ndidzakhala mosatekeseka nʼkumayangʼana pamalo anga okhala,*Ndidzachita zimenezi ngati kutentha komanso kuwala kwa dzuwa,Ngati mame amene amagwa pa nthawi yokolola, kukamatentha.
4 Chifukwa Yehova wandiuza kuti: “Ndidzakhala mosatekeseka nʼkumayangʼana pamalo anga okhala,*Ndidzachita zimenezi ngati kutentha komanso kuwala kwa dzuwa,Ngati mame amene amagwa pa nthawi yokolola, kukamatentha.