-
Yesaya 18:6Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
6 Onsewo adzasiyidwa kuti adyedwe ndi mbalame zamʼmapiri zodya nyama
Komanso nyama zakutchire zapadziko lapansi.
Mbalame zodya nyamazo zidzakhala zikuwadya nyengo yonse yachilimwe,
Ndipo nyama zonse zakutchire za padziko lapansi zidzakhala zikuwadya nthawi yonse yokolola.
-