-
Yesaya 19:2Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
2 “Ndidzachititsa kuti Aiguputo ayambane ndi Aiguputo anzawo.
Ndipo azidzamenyana okhaokha
Aliyense adzamenyana ndi mʼbale wake komanso munthu woyandikana naye.
Mzinda udzamenyana ndi mzinda unzake ndipo ufumu udzamenyana ndi ufumu unzake.
-