Yesaya 19:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Dziko la Yuda lidzakhala chinthu chochititsa mantha kwa Iguputo. Iwo akadzangomva wina akutchula dzikolo, adzachita mantha chifukwa cha zimene Yehova wa magulu ankhondo akumwamba wasakha kuti awachitire.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 19:17 Yesaya 1, ptsa. 203-204
17 Dziko la Yuda lidzakhala chinthu chochititsa mantha kwa Iguputo. Iwo akadzangomva wina akutchula dzikolo, adzachita mantha chifukwa cha zimene Yehova wa magulu ankhondo akumwamba wasakha kuti awachitire.+