-
Yesaya 19:19Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
19 Pa tsiku limenelo, pakatikati pa dziko la Iguputo padzakhala guwa lansembe la Yehova, ndipo mʼmalire mwake mudzakhala chipilala cha Yehova.
-