-
Yesaya 19:20Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
20 Zimenezi zidzakhala chizindikiro ndi umboni kwa Yehova wa magulu ankhondo akumwamba mʼdziko la Iguputo. Iwo adzalirira Yehova chifukwa cha anthu amene akuwapondereza, ndipo iye adzawatumizira mpulumutsi wamkulu amene adzawapulumutse.
-