-
Yesaya 20:6Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
6 Pa tsiku limenelo, anthu okhala mʼdziko limeneli lamʼmphepete mwa nyanja adzanena kuti, ‘Taonani zimene zachitikira dziko limene tinkalidalira lija, kumene tinathawirako kuti litithandize ndi kutipulumutsa kwa mfumu ya Asuri! Ndiye atipulumutse ndi ndani tsopano?’”
-