-
Yesaya 21:12Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
12 Mlondayo anayankha kuti:
“Mʼmawa ukubwera, ndipo usiku ukubweranso.
Ngati mukufuna kufunsa, funsani.
Ndipo mubwerenso.”
-