Yesaya 22:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Chifukwa Yehova wa magulu ankhondo akumwamba, Ambuye Wamkulu Koposa,Wabweretsa tsiku lachisokonezo, lakugonjetsedwa ndiponso lothetsa nzeru+MʼChigwa cha Masomphenya. Kumeneko mpanda ukugwetsedwa+Ndipo kufuula kopempha thandizo kukumveka mʼphiri. Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 22:5 Yesaya 1, ptsa. 234-235
5 Chifukwa Yehova wa magulu ankhondo akumwamba, Ambuye Wamkulu Koposa,Wabweretsa tsiku lachisokonezo, lakugonjetsedwa ndiponso lothetsa nzeru+MʼChigwa cha Masomphenya. Kumeneko mpanda ukugwetsedwa+Ndipo kufuula kopempha thandizo kukumveka mʼphiri.