Yesaya 22:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Kenako Yehova wa magulu ankhondo akumwamba anandiuza kuti: “‘Tchimo ili silidzakhululukidwa mpaka anthu inu mutafa,’+ akutero Yehova wa magulu ankhondo akumwamba, Ambuye Wamkulu Koposa.” Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 22:14 Yesaya 1, tsa. 238
14 Kenako Yehova wa magulu ankhondo akumwamba anandiuza kuti: “‘Tchimo ili silidzakhululukidwa mpaka anthu inu mutafa,’+ akutero Yehova wa magulu ankhondo akumwamba, Ambuye Wamkulu Koposa.”