-
Yesaya 22:18Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
18 Ndithu iye adzakukulunga mwamphamvu ndipo adzakuponyera mʼdziko lalikulu ngati akuponya mpira. Iweyo udzafera kumeneko ndipo magaleta ako ankhondo aulemerero adzakhala kumeneko. Zidzakhala zochititsa manyazi ku nyumba ya mbuye wako.
-