-
Yesaya 22:23Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
23 Ndidzamukhomerera ngati chikhomo pamalo okhalitsa. Iye adzakhala ngati mpando wachifumu waulemerero kunyumba ya bambo ake.
-