Yesaya 23:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Iwe mwana wamkazi wa Tarisi, sefukira mʼdziko lako ngati kusefukira kwa mtsinje wa Nailo. Kulibenso doko la sitima zapanyanja.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 23:10 Yesaya 1, tsa. 251
10 Iwe mwana wamkazi wa Tarisi, sefukira mʼdziko lako ngati kusefukira kwa mtsinje wa Nailo. Kulibenso doko la sitima zapanyanja.+